English | Chichewa | Chitumbuka

Parasite Street Science ndi chani?

#ParasiteStreetScience ndi ntchito imene inakhazikitsidwa kuthandizira anthu kuti adziwe zimene akuchita a zakafukufuku wa sayansi pa nkhani ya matenda a kashembe (amene amatchedwanso kaliodzera)

Ntchitoyi ikugwiridwa molumukizana pakati pa magulu a Wellcome Centre for Integrative Parasitology, University of Glasgow School of Life Sciences, Surge, Kamuzu University of Health Sciences ndi Malawi VOICES.

Ndalama zoyendetsera ntchitoyi zinachokera ku ScotPEN Wellcome Engagement Award (Wellcome Project Number 217078/Z/19/Z)

Zolembedwa Posachedwapa

Izi ndi nkhani ndimene zalembedwa ndi nyumba zina zofalitsa nkhani, pokamba za ntchito zathu

3 Aug 2022

Partick Thistle to host half-time educational street theatre performance

Partick Thistle will host a educational street theatre performance at half time of their game against Hamilton this weekend to raise awareness of infectious diseases in Africa...

Werengani
2 August 2022

Thistle to host educational street theatre performance this weekend

This Saturday, during the half time break of our game against Hamilton Academical, we will be hosting an educational street theatre performance...

Werengani
July 2021

2021 Parasite Street Science Performance

University of Glasgow and Surge present a 360˚ video from Parasite Street Science at Surge Festival 2021, in Glasgow, Scotland.

Werengani

Ma Program apa Wailesi

Awa ndi ena mwa nyumba zofalitsa nkhani zimene talumikizana nazo kuti zifalitse nkhani za zionetsero zathu ku Rumphi ndi ku Nkhotakota mu Malawi. Iwowa ankhala akukamba za ife pamene tikhale tikupanga zionetsero zathu kuthandizira kuti anthu amumadera ochuluka athenso kutenga nawo mbali mu zokambirana zathu. Ma wailesi awa athandizira kuti maprogram apezeke oti ticheze ndi magulu a anthu omvera Wailesi pamene titadzafunsane ndi kuyankhana mafunso.

Kamuzu University of Health Sciences
Malawi Ministry of Health
Malawi Liverpool Wellcome Trust
SURGE Scotland
University of Glasgow
Wellcome Centre for Integrative Parasitology